1 Mafumu 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ahabu atangomva kuti Naboti wafa, nthawi yomweyo ananyamuka n’kupita kumunda wa mpesa wa Naboti Myezereeli, kukautenga kuti ukhale wake.+
16 Ahabu atangomva kuti Naboti wafa, nthawi yomweyo ananyamuka n’kupita kumunda wa mpesa wa Naboti Myezereeli, kukautenga kuti ukhale wake.+