Miyambo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+ Miyambo 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndi anthu amene amakhala nthawi yaitali akumwa vinyo,+ amene amabwera kudzafunafuna vinyo wosakaniza.+ Hoseya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dama, vinyo wakale ndi vinyo wotsekemera zimawononga nzeru za munthu.+
20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+
30 Ndi anthu amene amakhala nthawi yaitali akumwa vinyo,+ amene amabwera kudzafunafuna vinyo wosakaniza.+