Yesaya 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+ Yesaya 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+
4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+
10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+