Salimo 139:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa.
16 Maso anu anandiona pamene ndinali mluza,+Ndipo ziwalo zanga zonse zinalembedwa m’buku lanu.M’bukumo munalembamo za masiku amene zinapangidwa+Koma panalibe ngakhale chiwalo chimodzi chimene chinali chitapangidwa.