Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+
12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+