Ekisodo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba+ kuti m’dziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.” Salimo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+ Mateyu 27:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kuyambira cha m’ma 12 koloko masana* kunagwa mdima+ m’dziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+
21 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba+ kuti m’dziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.”
11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+