Chivumbulutso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+
12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+