Yesaya 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+ Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+ Zekariya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fulumirani! Fulumirani anthu inu! Thawani m’dziko la kumpoto,”+ watero Yehova. “Anthu inu, ndinakubalalitsirani kutali kumbali zonse za dziko lapansi,”*+ watero Yehova. Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.
5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+
6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+
6 “Fulumirani! Fulumirani anthu inu! Thawani m’dziko la kumpoto,”+ watero Yehova. “Anthu inu, ndinakubalalitsirani kutali kumbali zonse za dziko lapansi,”*+ watero Yehova.
4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.