Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+ Aroma 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza pamene tinali ofooka,+ Khristu anafera anthu osapembedza Mulungu pa nthawi yoikidwiratu.+ Aroma 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti monga mwa kusamvera kwa munthu mmodziyo, ambiri+ anakhala ochimwa, momwemonso kudzera mwa kumvera+ kwa munthu mmodziyu, ambiri+ adzakhala olungama.+
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
19 Pakuti monga mwa kusamvera kwa munthu mmodziyo, ambiri+ anakhala ochimwa, momwemonso kudzera mwa kumvera+ kwa munthu mmodziyu, ambiri+ adzakhala olungama.+