Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+ Miyambo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, mvetsera mawu anga.+ Tchera khutu lako ku zonena zanga.+
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+