Salimo 105:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene anati: “Ndidzakupatsa dziko la Kanani+Kuti likhale gawo la cholowa chako.”+ Salimo 135:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dziko lawo analipereka kukhala cholowa,+Cholowa cha anthu ake Aisiraeli.+ Yeremiya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “M’masiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli,+ ndipo onse+ adzatuluka m’dziko la kumpoto ndi kulowa m’dziko limene ndinapereka kwa makolo anu monga cholowa chawo.+
18 “M’masiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli,+ ndipo onse+ adzatuluka m’dziko la kumpoto ndi kulowa m’dziko limene ndinapereka kwa makolo anu monga cholowa chawo.+