Yesaya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Isiraeli ndiponso Mpulumutsi wako.+ Ndapereka Iguputo monga dipo* lokuwombolera.+ Ndaperekanso Itiyopiya+ ndi Seba m’malo mwako.
3 Pakuti ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Isiraeli ndiponso Mpulumutsi wako.+ Ndapereka Iguputo monga dipo* lokuwombolera.+ Ndaperekanso Itiyopiya+ ndi Seba m’malo mwako.