Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.* Salimo 132:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ansembe anu avale chilungamo,+Ndipo okhulupirika anu afuule mosangalala.+
14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*