Salimo 98:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+ Yesaya 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo changa chili pafupi.+ Chipulumutso+ chochokera kwa ine chili m’njira ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+ ndipo zidzadikira dzanja langa.+
2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+
5 Chilungamo changa chili pafupi.+ Chipulumutso+ chochokera kwa ine chili m’njira ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+ ndipo zidzadikira dzanja langa.+