Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+