Deuteronomo 28:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+ Ezekieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+
63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+
6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+