Zekariya 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 A nyumba ya Efuraimu adzakhala ngati munthu wamphamvu+ ndipo adzasangalala mumtima mwawo ngati kuti amwa vinyo.+ Ana awo aamuna adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+ Mitima yawo idzakondwera chifukwa cha Yehova.+
7 A nyumba ya Efuraimu adzakhala ngati munthu wamphamvu+ ndipo adzasangalala mumtima mwawo ngati kuti amwa vinyo.+ Ana awo aamuna adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+ Mitima yawo idzakondwera chifukwa cha Yehova.+