1 Mafumu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Solomo anaimirira kutsogolo kwa guwa lansembe+ la Yehova pamaso pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+ Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+
22 Tsopano Solomo anaimirira kutsogolo kwa guwa lansembe+ la Yehova pamaso pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+