1 Akorinto 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwachitsanzo, mwa mzimu wina amapatsidwa mawu anzeru,+ ndipo wina amapatsidwa mawu ozindikira+ mwa mzimu womwewo. Aefeso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru+ ndi kuti mumvetse zimene Iye akuulula mogwirizana ndi kumudziwa molondola.+
8 Mwachitsanzo, mwa mzimu wina amapatsidwa mawu anzeru,+ ndipo wina amapatsidwa mawu ozindikira+ mwa mzimu womwewo.
17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru+ ndi kuti mumvetse zimene Iye akuulula mogwirizana ndi kumudziwa molondola.+