2 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo, wosamvera malamuloyo adzaonekera ndithu, amene Ambuye Yesu adzamuthetsa ndi mzimu wa m’kamwa mwake,+ pomuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+ Chivumbulutso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ulape.+ Ngati sulapa, ndikubwera kwa iwe msanga, ndipo ndidzamenyana+ nawo ndi lupanga lalitali la m’kamwa mwanga.+
8 Pamenepo, wosamvera malamuloyo adzaonekera ndithu, amene Ambuye Yesu adzamuthetsa ndi mzimu wa m’kamwa mwake,+ pomuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+
16 Choncho ulape.+ Ngati sulapa, ndikubwera kwa iwe msanga, ndipo ndidzamenyana+ nawo ndi lupanga lalitali la m’kamwa mwanga.+