Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+ Yesaya 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 N’chifukwa chake temberero lameza dzikolo,+ ndipo anthu okhala m’dzikolo apezeka ndi mlandu. Chotero anthu okhala m’dzikolo achepamo, ndipo anthu amene atsalamo ndi ochepa kwambiri.+ Yeremiya 51:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Babulo adzakhala milu yamiyala+ ndi malo obisalamo mimbulu.+ Adzakhala chinthu chodabwitsa ndi chochiimbira mluzu ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.+ Chivumbulutso 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu,+ akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo okhala ziwanda, ndiponso obisalamo mpweya+ uliwonse wonyansa wotuluka m’kamwa, komanso obisalamo mbalame iliyonse yonyansa ndi yodedwa.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
6 N’chifukwa chake temberero lameza dzikolo,+ ndipo anthu okhala m’dzikolo apezeka ndi mlandu. Chotero anthu okhala m’dzikolo achepamo, ndipo anthu amene atsalamo ndi ochepa kwambiri.+
37 Babulo adzakhala milu yamiyala+ ndi malo obisalamo mimbulu.+ Adzakhala chinthu chodabwitsa ndi chochiimbira mluzu ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.+
2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu,+ akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo okhala ziwanda, ndiponso obisalamo mpweya+ uliwonse wonyansa wotuluka m’kamwa, komanso obisalamo mbalame iliyonse yonyansa ndi yodedwa.+