Numeri 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni. Deuteronomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+
28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni.
9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+