-
2 Mafumu 3:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno Aisiraeliwo anayamba kugwetsa mizinda.+ Pamalo alionse abwino, aliyense anali kuponyapo mwala mpaka kudzaza malo onsewo. Anatseka kasupe aliyense wamadzi+ ndi kugwetsa mtengo uliwonse wabwino.+ Koma miyala ya mzinda wa Kiri-hareseti+ yokha anaisiya. Oponya miyala anazungulira mzindawo n’kuuponya miyala.
-