Ekisodo 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+ Miyambo 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Woipa amatenga chiphuphu mobisa,+ kuti akhotetse njira za chiweruzo.+
8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+