1 Mbiri 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nenani kuti: ‘Tipulumutseni, inu Mulungu wachipulumutso chathu,+Tisonkhanitseni pamodzi ndi kutilanditsa kwa anthu a mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+ ndiponso kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+ Salimo 65:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mudzatiyankha ndi zinthu zochititsa mantha zochitika mwachilungamo,+Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Inu Chidaliro cha malire onse a dziko lapansi ndi anthu okhala pafupi ndi nyanja zakutali.+ Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+ Habakuku 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndidzakondwerabe mwa Yehova+ ndipo ndidzasangalala mwa Mulungu wachipulumutso changa.+ Chivumbulutso 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+
35 Nenani kuti: ‘Tipulumutseni, inu Mulungu wachipulumutso chathu,+Tisonkhanitseni pamodzi ndi kutilanditsa kwa anthu a mitundu ina,+Kuti titamande dzina lanu loyera,+ ndiponso kuti tilankhule mokondwa pokutamandani.+
5 Mudzatiyankha ndi zinthu zochititsa mantha zochitika mwachilungamo,+Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Inu Chidaliro cha malire onse a dziko lapansi ndi anthu okhala pafupi ndi nyanja zakutali.+
9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+