Yeremiya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno n’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira ya ku Iguputo+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Sihori?+ N’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira yopita kudziko la Asuri+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Firate?
18 Ndiyeno n’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira ya ku Iguputo+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Sihori?+ N’chifukwa chiyani ukufuna kuyenda m’njira yopita kudziko la Asuri+ kuti ukamwe madzi a mumtsinje wa Firate?