Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ Miyambo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali m’badwo umene umadziona kuti ndi woyera,+ koma sunasambe kuti uchotse ndowe zake.+
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+