Yeremiya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+
6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+