2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo. Yeremiya 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+
6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo.
33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+