1 Yohane 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikanena kuti: “Tilibe uchimo,”+ ndiye kuti tikudzinamiza+ ndipo mwa ife mulibe choonadi.