Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+ Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova. Yeremiya 50:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Zungulirani Babulo ndi kumuukira kuchokera kumbali zonse,+ inu nonse odziwa kukunga uta.+ Mulaseni+ ndipo musasunge muvi uliwonse, pakuti iye wachimwira Yehova.+ Yeremiya 50:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+ Danieli 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kumasulira kwa mawuwa ndi uku: MENE, Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo waumaliza.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova.
14 “Zungulirani Babulo ndi kumuukira kuchokera kumbali zonse,+ inu nonse odziwa kukunga uta.+ Mulaseni+ ndipo musasunge muvi uliwonse, pakuti iye wachimwira Yehova.+
27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+