Yeremiya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+ Yeremiya 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse aneneri. Anali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, koma inu simunawamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+ Yeremiya 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+
13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+
4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse aneneri. Anali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, koma inu simunawamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+
33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+