Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Yeremiya 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino,+ ndipo ndidzawabwezeretsa kudziko lino.+ Pamenepo ndidzawalimbitsa, osati kuwapasula. Ndidzawabzala, osati kuwazula.+ Yeremiya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwanira muli ku Babulo ndidzakucheukirani anthu inu,+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa lokubwezeretsani kumalo ano.’+
85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+
6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino,+ ndipo ndidzawabwezeretsa kudziko lino.+ Pamenepo ndidzawalimbitsa, osati kuwapasula. Ndidzawabzala, osati kuwazula.+
10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwanira muli ku Babulo ndidzakucheukirani anthu inu,+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa lokubwezeretsani kumalo ano.’+