15 Atatsiriza kudya chakudya cham’mawacho, Yesu anafunsa Simoni Petulo kuti: “Simoni mwana wa Yohane, kodi umandikonda ine kuposa izi?”+ Iye anamuyankha kuti: “Inde Ambuye, inunso mukudziwa kuti ndimakukondani kwambiri.”+ Iye anamuuza kuti: “Dyetsa ana a nkhosa anga.”+