Salimo 75:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+ Salimo 82:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pulumutsani munthu wonyozeka ndi wosauka.+Alanditseni m’manja mwa anthu oipa.”+ Miyambo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+
10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+
21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+