Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko. Yeremiya 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+
10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.
8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+