Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+ Yeremiya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iwe, ukufunafunabe zinthu zazikulu.+ Leka kuzifunafuna.”’+ “‘Anthu onse ndikuwagwetsera tsoka+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako monga chofunkha chako kulikonse kumene ungapite,’ watero Yehova.”+
9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+
5 Koma iwe, ukufunafunabe zinthu zazikulu.+ Leka kuzifunafuna.”’+ “‘Anthu onse ndikuwagwetsera tsoka+ ndipo iwe ndidzakupatsa moyo wako monga chofunkha chako kulikonse kumene ungapite,’ watero Yehova.”+