1 Mbiri 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+ Salimo 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+ Salimo 37:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+ Salimo 84:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova wa makamu, wodala ndi munthu amene amakhulupirira inu.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+
3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+
40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+