Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.” Yoswa 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.