Deuteronomo 32:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Milungu imene inali kudya mafuta a nsembe zawo,+Ndi kumwa vinyo wa nsembe zawo zachakumwa?+Ibwere kudzakuthandizani.+Ikhaletu malo anu obisalamo.+ Yeremiya 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+
38 Milungu imene inali kudya mafuta a nsembe zawo,+Ndi kumwa vinyo wa nsembe zawo zachakumwa?+Ibwere kudzakuthandizani.+Ikhaletu malo anu obisalamo.+
18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+