2 Mafumu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+
7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+