Nahumu 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Magaleta awo ankhondo akuyenda mothamanga kwambiri m’misewu.+ Iwo akuthamangira uku ndi uku m’mabwalo a mzinda, ndipo akuoneka ngati zounikira zamoto. Magaletawo akuderukaderuka ngati mphezi.+
4 Magaleta awo ankhondo akuyenda mothamanga kwambiri m’misewu.+ Iwo akuthamangira uku ndi uku m’mabwalo a mzinda, ndipo akuoneka ngati zounikira zamoto. Magaletawo akuderukaderuka ngati mphezi.+