Obadiya 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kodi akuba atabwera kwa iwe, kapena olanda zinthu atabwera kwa iwe usiku, angasakaze kufikira pati?+ Kodi sakhoza kungoba zimene akufuna? Kapena kodi okolola mphesa atabwera kwa iwe, sangasiyeko zina zoti munthu angathe kukunkha?+
5 “Kodi akuba atabwera kwa iwe, kapena olanda zinthu atabwera kwa iwe usiku, angasakaze kufikira pati?+ Kodi sakhoza kungoba zimene akufuna? Kapena kodi okolola mphesa atabwera kwa iwe, sangasiyeko zina zoti munthu angathe kukunkha?+