Machitidwe 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+
4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+