Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+ Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+
6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+
11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+