Yesaya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+ Yesaya 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pali amene akutiwombola.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ Woyera wa Isiraeli.”+
13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+