Yeremiya 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani, muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikukutumizirani pakati panu.”’+ Danieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+
27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani, muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikukutumizirani pakati panu.”’+
4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+