-
Malaki 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Aliyense wochita zachinyengo popereka nsembe nyama yachilema ndi wotembereredwa. Iye amalonjeza ndi kupereka nsembe nyama yachilema kwa Yehova pamene nyama yamphongo yabwinobwino, ali nayo pagulu la ziweto zake.+ Ine ndine Mfumu yaikulu+ ndipo dzina langa lidzaopedwa pakati pa anthu a mitundu ina,”+ watero Yehova wa makamu.
-