Yeremiya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo ndinati: “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Aneneri akuuza anthuwo kuti, ‘Lupanga silidzakukanthani, ndipo njala yaikulu sidzakugwerani, koma Mulungu adzakupatsani mtendere weniweni m’malo ano.’”+ Yeremiya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+ Ezekieli 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+ 1 Atesalonika 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+
13 Pamenepo ndinati: “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Aneneri akuuza anthuwo kuti, ‘Lupanga silidzakukanthani, ndipo njala yaikulu sidzakugwerani, koma Mulungu adzakupatsani mtendere weniweni m’malo ano.’”+
17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+
10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+
3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+