2 Samueli 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu. Miyambo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+ Yeremiya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Aliyense wa inu asamale ndi mnzake,+ ndipo musakhulupirire m’bale aliyense.+ Pakuti munthu aliyense amalanda malo a m’bale wake,+ ndipo munthu aliyense amakhala akuyendayenda kunenera mnzake miseche.+
27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.
19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+
4 “Aliyense wa inu asamale ndi mnzake,+ ndipo musakhulupirire m’bale aliyense.+ Pakuti munthu aliyense amalanda malo a m’bale wake,+ ndipo munthu aliyense amakhala akuyendayenda kunenera mnzake miseche.+